Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 90:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku a zaka zathu ndiwo zaka makumi asanu ndi awiri,Kapena tikakhala nayo mphamvudi zaka makumi asanu ndi atatu;Koma teronso kukula kwao kumati cibvuto ndi copanda pace;Pakuti kumapitako msanga ndipo tithawa ife tomwe.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 90

Onani Masalmo 90:10 nkhani