Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 90:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ambuye, Inu munatikhalira mokhalamoM'mibadwo mibadwo.

2. Asanabadwe mapiri,Kapena musanalenge dziko lapansi, ndi lokhalamo anthu,Inde, kuyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha,Inu ndinu Mulungu.

3. Mubweza munthu akhale pfumbi;Nimuti, Bwererani inu, ana a anthu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 90