Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 9:17-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Oipawo adzabwerera kumanda,Inde amitundu onse akuiwala Mulungu.

18. Pakuti sadzaiwalika nthawi zonse waumphawi,Kapena ciyembekezo ca ozunzika sicidzaonongeka kosatha.

19. Ukani, Yehova, asalimbike munthu;Amitundu aweruzidwe pankhope panu.

20. Muwacititse mantha, Yehova; Adziwe amitundu kuti ali anthu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 9