Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 88:15-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Wozunzika ine ndi wofuna kufa kuyambira ubwana wanga;Posenza zoopsa zanu, ndithedwa nzeru.

16. Kuzaza kwanu kwandimiza;Zoopsa zanu zinandiononga,

17. Zinandizungulira ngati madzi tsiku lonse;Zinandizinga pamodzi.

18. Munandicotsera kutali wondikonda ndi bwenzi langa,Odziwana nane akhala kumdima.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 88