Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 88:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, Mulungu wa cipulumutso canga,Ndinapfuula pamaso panu usana ndi usiku,

2. Pemphero langa lidze pamaso panu;Mundicherere khutu kukuwa kwanga:

3. Pakuti mzimu wanga wadzala nao mabvuto,Ndi moyo wanga wayandikira kumanda.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 88