Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 76:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Inu ndinu wakuunikira, ndi womveka wakuposa mapiri muli acifwamba.

5. Olimba mtima cifunkhidwa cuma cao, agona tulo tao;Amuna onse amphamvu asowa manja ao.

6. Pa kudzudzula kwanu, Mulungu wa Yakobo,Gareta ndi kavalo yemwe anagwa m'tulo.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 76