Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 67:3-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Anthu akuyamikeni, Mulungu;Anthu onse akuyamikeni.

4. Anthu akondwere, napfuule makondwera;Pakuti mudzaweruza anthu malunjika,Ndipo mudzalangiza anthu pa dziko lapansi.

5. Anthu akuyamikeni, Mulungu;Anthu onse akuyamikeni.

6. Dziko lapansi lapereka zipatso zace:Mulungu, Mulungu wathu adzatidalitsa.

7. Mulungu adzatidalitsa;Ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzamuopa Iye,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 67