Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 64:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Adzawakhumudwitsa, lilime lao lidzawatsutsa;Onse akuwaona adzawathawa.

9. Ndipo anthu onse adzacita mantha;Nadzabukitsa cocita Mulungu,Nadzasamalira nchito yace.

10. Wolungama adzakondwera mwa Yehova, nadzakhulupirira Iye;Ndipo oongoka mtima onse adzalemekeza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 64