Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 6:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndalema nako kuusa moyo kwanga;Ndiyandamitsa kama wanga usiku wonse;Mphasa yanga ndiolobza ndi misozi yanga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 6

Onani Masalmo 6:6 nkhani