Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 6:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, musandidzudzule mu mkwiyo wanu,Ndipo musandilange m'ukali wanu.

2. Mundicitire cifundo, Yehova; pakuti ndalefuka ine:Mundicize, Yehova; pakuti anthunthumira mafupa anga.

3. Moyo wanganso wanthunthumira kwakukuru;Ndipo Inu, Yehova, kufikira liti?

Werengani mutu wathunthu Masalmo 6