Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 58:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Kodi muli cete ndithu poyenera inu kunena zolungama?Muweruza ana a anthu molunjika kodi?

2. Inde, mumtima mucita zosalungama;Pa dziko lapansi mugawira anthu ciwawa ca m'manja mwanu.

3. Oipa acita cilendo cibadwire:Asokera kuyambira kubadwa kwao, nanena bodza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 58