Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 55:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Inu, Mulungu, mudzawatsitsira ku dzenje la cionongeko:Anthu okhetsa mwazi ndi acinyengo masiku ao sadzafikira nusu;Koma ine ndidzakhulupirira Inu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 55

Onani Masalmo 55:23 nkhani