Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 55:22-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Umsenze Yehova nkhawa zako, ndipo Iyeadzakugwiriziza:Nthawi zonse sadzalola wolungama agwedezeke.

23. Koma Inu, Mulungu, mudzawatsitsira ku dzenje la cionongeko:Anthu okhetsa mwazi ndi acinyengo masiku ao sadzafikira nusu;Koma ine ndidzakhulupirira Inu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 55