Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 50:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mulungu wa milungu, Yehova, wanena,Aitana dziko lapansi kuyambira kuturuka kwa dzuwa kufikira kulowa kwace.

2. Mulungu awalira m'Ziyoni, mokongola mwangwiro.

3. Adzafika Mulungu wathu, ndipo sadzakhala cete:Moto udzanyeka pankhope pace,Ndipo pozungulira pace padzasokosera kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 50