Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 49:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Dzamveni kuno, anthu inu nonse;Cherani khutu, inu nonse amakono,

2. Awamba ndi omveka omwe,Acuma ndi aumphawi omwe.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 49