Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 46:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mulungu ndiye pothawirapo pathu ndi mphamvu yathu,Thandizo lopezekeratu m'masautso.

2. Cifukwa cace sitidzacita mantha, lingakhale lisandulika dziko lapansi,Angakhale mapiri asunthika, nakhala m'kati mwa nyanja;

Werengani mutu wathunthu Masalmo 46