Inu munapitikitsa amitundu ndi dzanja lanu, koma iwowa munawaoka;Munasautsa mitundu ya anthu, ndipo munawaingitsa,