Mulungu, tidamva m'makutu mwathu, makolo athu anatisimbira,Za nchitoyo mudaicita masiku ao, masiku akale.