Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 41:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Umo ndidziwa kuti mukondwera ndi ine,Popeza mdani wanga sandiseka.

12. Ndipo ine, mundigwirizize m'ungwiro wanga,Ndipo mundiike pankhope panu ku nthawi yamuyaya.

13. Wodalitsika Yehova, Mulungu wa Israyeli,Kucokera nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha.Amen, ndi Amen.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 41