Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 38:18-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Pakuti ndidzafotokozera mphulupulu yanga;Nditenga nkhawa cifukwa ca chimo langa.

19. Koma adani anga ali ndi moyo, nakhalandi mphamvu:Ndipo akundida kopanda cifukwa acuruka.

20. Ndipo iwo akubwezera coipa pa cabwinoAtsutsana nane, popeza nditsata cabwino.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 38