Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 38:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, musandidzudzule ndi mkwiyo wanu:Ndipo musandilange moopsa m'mtima mwanu.

2. Pakuti mibvi yanu yandilowa,Ndi dzanja lanu landigwera.

3. Mumnofu mwanga mulibe camoyo cifukwa ca ukali wanu;Ndipo m'mafupa anga simuzizira, cifukwa ca colakwa canga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 38