Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 37:26-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Tsiku lonse acitira cifundo, nakongoletsa;Ndipo mbumba zace zidalitsidwa.

27. Siyana naco coipa, nucite cokoma,Nukhale nthawi zonse.

28. Pakuti Yehova akonda ciweruzo,Ndipo sataya okondedwa ace:Asungika kosatha:Koma adzadula mbumba za oipa.

29. Olungama adzalandira dziko lapansi,Nadzakhala momwemo kosatha.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 37