Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 32:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinabvomera coipa canga kwa Inu;Ndipo mphulupulu yanga sindinaibisa.Ndinati, Ndidzaululira Yehova macimo anga;Ndipo munakhululukira coipa ca kulakwa kwanga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 32

Onani Masalmo 32:5 nkhani