Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 29:10-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Yehova anakhala pa Cigumula:Inde Yehova akhala mfumu ku nthawi yomka muyaya.

11. Yehova adzapatsa anthu ace mphamvu:Yehova adzadalitsa anthu ace ndi mtendere.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 29