Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 29:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Liu la Yehova liswetsa nyama zazikazi,Ndipo lipulula nkhalango:Ndipo m'Kacisi mwace zonse ziri m'mwemo zimati, Ulemerero:

Werengani mutu wathunthu Masalmo 29

Onani Masalmo 29:9 nkhani