Kwa Inu, Yehova, ndidzapfuulira;Thanthwe langa, musandikhalire ngati wosamva:Pakuti ngati munditontholera ine,Ndidzafanana nao iwo akutsikira kumanda.