Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 27:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cinthu cimodzi ndinacipempha kwa Yehova, ndidzacilondola ici:Kuti ndikhalitse m'nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,Kupenya kukongola kwace kwa Yehova ndi kufunsitsa m'Kacisi wace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 27

Onani Masalmo 27:4 nkhani