Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 20:7-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. Ena atama magareca, ndi ena akavalo:Koma ife tidzachula dzina la Yehova Mulungu wathu.

8. Iwowa anagonieka, nagwa:Koma ife tauka, ndipo takhala ciriri.

9. Yehova, pulumutsani,Mfumuyo atibvomereze tsiku lakuitana ife.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 20