Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi,Nacita upo akulu pamodzi,Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wace, ndi kuti.