Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 2:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Aphokoseranji amitundu.Nalingiriranji anthu zopanda pace?

2. Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi,Nacita upo akulu pamodzi,Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wace, ndi kuti.

3. Tidule zomangira zao,Titaye nsinga zao.

4. Wokhala m'mwambayo adzaseka;Ambuye adzawanyoza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 2