Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 18:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zidaoneka zoyendamo madzi,Nafukuka maziko a dziko lapansi,Mwa kudzudzula kwanu, Yehova,Mwa mpumo wa mpweya wa m'mphuno mwanu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 18

Onani Masalmo 18:15 nkhani