Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 16:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndisungeni ine, Mulungu: pakuti ndakhulupirira Inu.

2. Ndinati kwa Yehova, Inu ndinu Ambuye wanga:Ndiribe cabwino cina coposa Inu.

3. Za oyera mtima okhala pa dziko lapansi,Iwo ndiwo omveka mbiri, mwa iwowo muli cikondwero canga conse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 16