Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 15:4-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. M'maso mwace munthu woonongeka anyozeka;Koma awacitira ulemu akuopa Yehova.Atalumbira kwa tsoka lace, sasintha ai.

5. Ndarama zace sakongoletsa mofuna phindu lalikuru,Ndipo salandira cokometsera mlandu kutsutsa wosacimwa.Munthu wakucita izi sadzagwedezeka ku nthawi zonse,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 15