Ndarama zace sakongoletsa mofuna phindu lalikuru,Ndipo salandira cokometsera mlandu kutsutsa wosacimwa.Munthu wakucita izi sadzagwedezeka ku nthawi zonse,