Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 143:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Imvani pemphero langa, Yehova; ndicherere khutu kupemba kwanga;Ndiyankheni mwa cikhulupiriko canu, mwa cilungamo canu.

2. Ndipo musaitane mlandu wa mtumiki wanu;Pakuti pamaso panu sipadzakhala wolungama wamoyo mmodzi yense.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 143