Tamverani kupfuula kwanga; papeza ndisauka kwambiri;Ndilanditseni kwa iwo akundilondola; popeza andilaka.