Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 140:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Munthu wamlomo sadzakhazikika pa dziko lapansi;Coipa cidzamsaka munthu waciwawa kuti cimgwetse.

12. Ndidziwa kuti Yehova adzanenera wozunzika mlandu,Ndi kuweruzira aumphawi,

13. Indedi, olungama adzayamika dzina lanu;Oongoka mtima adzakhala pamaso panu,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 140