Ndisanaumbidwe ine maso anu anandipenya,Ziwalo zanga zonse zinalembedwa m'buku mwanu,Masiku akuti ziumbidwe, Pakalibe cimodzi ca izo.