Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 136:22-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Cosiyira ca kwa Israyeli mtumiki wace;Pakuti cifundo cace ncosatha.

23. Amene anatikumbukila popepuka ife;Pakuti cifundo cace ncosatha.

24. Natikwatula kwa otisautsa;Pakuti cifundo cace ncosatha.

25. Ndiye wakupatsa nyama zonse cakudya;Pakuti cifundo cace ncosatha.

26. Yamikani Mulungu wa kumwamba,Pakuti cifundo cace ncosatha.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 136