Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 132:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, kumbukilani Davide Kuzunzika kwace konse;

2. Kuti analumbira Yehova,Nawindira Wamphamvuyo wa Yakobo, ndi kuti,

3. Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga,Ngati ndidzakwera pa kama logonapo;

4. Ngati ndidzalola maso anga agone,Kapena zikope zanga ziodzere;

Werengani mutu wathunthu Masalmo 132