Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 132:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, kumbukilani Davide Kuzunzika kwace konse;

2. Kuti analumbira Yehova,Nawindira Wamphamvuyo wa Yakobo, ndi kuti,

3. Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga,Ngati ndidzakwera pa kama logonapo;

Werengani mutu wathunthu Masalmo 132