Ndidzacita uphungu m'moyo mwanga kufikira liti,Pokhala ndi cisoni m'mtima mwanga tsiku lonse?Adzandiukira ine mdani wanga kufikira liti?