Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 129:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga,Anene tsono Israyeli;

2. Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga;Koma sanandilaka.

3. Olima analima pamsana panga;Anatalikitsa mipere yao.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 129