Mkazi wako adzanga mpesa wopatsa m'mbali za nyumba yako;Ana ako adzanga timitengo ta azitona pozinga podyera pako.