Pamenepo pakamwa pathu panadzala ndi kuseka,Ndi lilime lathu linapfuula mokondwera;Pamenepo anati mwa amitundu,Yehova anawacitira iwo zazikuru,