Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 109:9-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Ana ace akhale amasiye, Ndi mkazi wace wamasiye.

10. Ana ace akhale amcirakuyenda ndi opemphapempha;Afunefune zosowa zao kucokera m'mabwinja mwao.

11. Wokongoletsa agwire zonse ali nazo;Ndi alendo alande za nchito yace.

12. Pasakhale munthu wakumdtira cifundo;Kapena kucitira cokoma ana ace amasiye.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 109