Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 109:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Ndamuka ngati mthunzi womka m'taliNdiingidwa kwina ndi kwina ngati dzombe.

24. Mabondo anga agwedezeka cifukwa ca kusala;Ndi mnofu wanga waonda posowa mafuta.

25. Ndiwakhaliranso cotonza;Pakundiona apukusa mutu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 109