Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 109:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mulungu wa cilemekezo canga, musakhale cete;

2. Pakuti pakamwa pa woipa ndi pakamwa pa cinyengo pananditsegukira;Anandilankhulira ndi m'kamwa mwa bodza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 109