Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 104:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Lemekeza Yehova, moyo wanga;Yehova, Mulungu wanga, Inu ndinu wamkurukuru;

2. Mubvala ulemu ndi cifumu.Amene mudzikuta nako kuunika monga ndi cobvala;Ndi kuyala thambo ngati nsaru yocinga;

3. Amene alumikiza mitanda ya zipinda zace m'madzi;Naika makongwa akhale agareta ace;Nayenda pa mapiko a mphepo;

Werengani mutu wathunthu Masalmo 104