Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 103:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Lemekeza Yehova, moyo wanga;Ndi zonse za m'kati mwanga zilemekeze dzina lace loyera.

2. Lemekeza Yehova, moyo wanga,Ndi kusaiwala zokoma zace zonse aticitirazi:

3. Amene akhululukira mphulupulu zako zonse;Naciritsa nthenda zako zonse;

Werengani mutu wathunthu Masalmo 103